CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 27-28
Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Zovala za Ansembe?
Zovala za ansembe a ku Isiraeli zimatikumbutsa kufunika kofufuza kuti tidziwe zimene Yehova amafuna, kukhala oyera komanso kuchita zinthu mwaulemu.
Kodi tingafufuze bwanji kuti tidziwe zimene Yehova amafuna?
Kodi kukhala oyera kumatanthauza chiyani?
Kodi tingatani kuti tizisonyeza ulemu?