Genesis 36:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Timina anali mkazi wamngʼono wa Elifazi mwana wa Esau. Patapita nthawi, Timina anaberekera Elifazi mwana wamwamuna dzina lake Amaleki.+ Ana a Ada mkazi wa Esau anali amenewa.
12 Timina anali mkazi wamngʼono wa Elifazi mwana wa Esau. Patapita nthawi, Timina anaberekera Elifazi mwana wamwamuna dzina lake Amaleki.+ Ana a Ada mkazi wa Esau anali amenewa.