Genesis 36:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Elifazi mwana wa Esau anali ndi mdzakazi dzina lake Timina.+ Patapita nthawi, mdzakaziyu anaberekera Elifazi mwana wamwamuna dzina lake Amaleki.+ Amenewa ndiwo anali ana a Ada mkazi wa Esau.
12 Elifazi mwana wa Esau anali ndi mdzakazi dzina lake Timina.+ Patapita nthawi, mdzakaziyu anaberekera Elifazi mwana wamwamuna dzina lake Amaleki.+ Amenewa ndiwo anali ana a Ada mkazi wa Esau.