Genesis 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kutacha mʼmawa, Yakobo anadabwa kuona kuti ali ndi Leya. Ataona zimenezi anafunsa Labani kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwandichitira zimenezi? Ine ndakugwirirani ntchito kuti mundipatse Rakele. Nanga nʼchifukwa chiyani mwandipusitsa chonchi?”+
25 Kutacha mʼmawa, Yakobo anadabwa kuona kuti ali ndi Leya. Ataona zimenezi anafunsa Labani kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwandichitira zimenezi? Ine ndakugwirirani ntchito kuti mundipatse Rakele. Nanga nʼchifukwa chiyani mwandipusitsa chonchi?”+