Genesis 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma kutacha m’mawa, Yakobo anadabwa kuona kuti ali ndi Leya! Ataona zimenezi anakafunsa Labani kuti: “Ndiye chiyani mwachitachi? Kodi si Rakele amene ndakugwirirani ntchito? N’chifukwa chiyani mwandipusitsa chonchi?”+
25 Koma kutacha m’mawa, Yakobo anadabwa kuona kuti ali ndi Leya! Ataona zimenezi anakafunsa Labani kuti: “Ndiye chiyani mwachitachi? Kodi si Rakele amene ndakugwirirani ntchito? N’chifukwa chiyani mwandipusitsa chonchi?”+