Genesis 31:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho Labani anakalowa mutenti ya Yakobo ndi mutenti ya Leya, ndiponso mutenti ya akapolo aakazi awiri aja,+ koma sanaipeze. Potsirizira pake, anatuluka mutenti ya Leya nʼkukalowa mutenti ya Rakele.
33 Choncho Labani anakalowa mutenti ya Yakobo ndi mutenti ya Leya, ndiponso mutenti ya akapolo aakazi awiri aja,+ koma sanaipeze. Potsirizira pake, anatuluka mutenti ya Leya nʼkukalowa mutenti ya Rakele.