Genesis 31:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pamenepo Labani anakalowa muhema wa Yakobo, ndi muhema wa Leya, ndiponso muhema wa akapolo aakazi awiri aja,+ koma sanaipeze. Potsirizira pake, anatuluka muhema wa Leya n’kukalowa muhema wa Rakele.
33 Pamenepo Labani anakalowa muhema wa Yakobo, ndi muhema wa Leya, ndiponso muhema wa akapolo aakazi awiri aja,+ koma sanaipeze. Potsirizira pake, anatuluka muhema wa Leya n’kukalowa muhema wa Rakele.