Ekisodo 31:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chimenechi nʼchizindikiro pakati pa ine ndi Aisiraeli mpaka kalekale,+ chifukwa mʼmasiku 6, Yehova anapanga kumwamba ndi dziko lapansi, koma pa tsiku la 7 anapuma pa ntchito yake ndipo anasangalala.’”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:17 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2019, tsa. 3 Kukambitsirana, tsa. 345
17 Chimenechi nʼchizindikiro pakati pa ine ndi Aisiraeli mpaka kalekale,+ chifukwa mʼmasiku 6, Yehova anapanga kumwamba ndi dziko lapansi, koma pa tsiku la 7 anapuma pa ntchito yake ndipo anasangalala.’”+