Ekisodo 31:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chimenechi n’chizindikiro pakati pa ine ndi ana a Isiraeli mpaka kalekale,+ chifukwa m’masiku 6, Yehova anapanga kumwamba ndi dziko lapansi, ndipo pa tsiku la 7 anapuma pa ntchito yake.’”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:17 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2019, tsa. 3 Kukambitsirana, tsa. 345
17 Chimenechi n’chizindikiro pakati pa ine ndi ana a Isiraeli mpaka kalekale,+ chifukwa m’masiku 6, Yehova anapanga kumwamba ndi dziko lapansi, ndipo pa tsiku la 7 anapuma pa ntchito yake.’”+