Levitiko 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musamachite zinthu zimene anthu a ku Iguputo kumene munkakhala amachita, komanso musamachite zinthu zimene anthu amʼdziko la Kanani limene ndikukupititsani amachita.+ Ndipo musamakatsatire malamulo awo.
3 Musamachite zinthu zimene anthu a ku Iguputo kumene munkakhala amachita, komanso musamachite zinthu zimene anthu amʼdziko la Kanani limene ndikukupititsani amachita.+ Ndipo musamakatsatire malamulo awo.