Levitiko 27:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 wansembe azimuwerengera mtengo wake, mogwirizana ndi zaka zimene zatsala kuti Chaka cha Ufulu chifike, ndipo tsiku lomwelo azipereka mtengo umene wansembe wawerengerawo.+ Ndalamazo ndi zopatulika kwa Yehova.
23 wansembe azimuwerengera mtengo wake, mogwirizana ndi zaka zimene zatsala kuti Chaka cha Ufulu chifike, ndipo tsiku lomwelo azipereka mtengo umene wansembe wawerengerawo.+ Ndalamazo ndi zopatulika kwa Yehova.