Levitiko 27:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 wansembe azimuwerengera mtengo wake, malinga ndi zaka zimene zatsala kuti Chaka cha Ufulu chifike, ndipo tsiku lomwelo azipereka mtengo umene wansembe wawerengerawo.+ Ndalamazo ndi zopatulika kwa Yehova.+
23 wansembe azimuwerengera mtengo wake, malinga ndi zaka zimene zatsala kuti Chaka cha Ufulu chifike, ndipo tsiku lomwelo azipereka mtengo umene wansembe wawerengerawo.+ Ndalamazo ndi zopatulika kwa Yehova.+