Numeri 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kuchigwa cha Esikolo,*+ anadula nthambi yokhala ndi phava limodzi lalikulu la mphesa, ndipo anthu awiri analinyamula paphewa ndi ndodo yonyamulira. Anatengakonso makangaza* ndi nkhuyu.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:23 Nsanja ya Olonda,6/15/2006, tsa. 16
23 Atafika kuchigwa cha Esikolo,*+ anadula nthambi yokhala ndi phava limodzi lalikulu la mphesa, ndipo anthu awiri analinyamula paphewa ndi ndodo yonyamulira. Anatengakonso makangaza* ndi nkhuyu.+