Numeri 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kuchigwa* cha Esikolo,+ anadula nthambi yokhala ndi tsango limodzi la mphesa,+ ndipo anthu awiri analinyamula paphewa ndi mitengo yonyamulira. Anatengakonso makangaza*+ ndi nkhuyu. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:23 Nsanja ya Olonda,6/15/2006, tsa. 16
23 Atafika kuchigwa* cha Esikolo,+ anadula nthambi yokhala ndi tsango limodzi la mphesa,+ ndipo anthu awiri analinyamula paphewa ndi mitengo yonyamulira. Anatengakonso makangaza*+ ndi nkhuyu.