-
Numeri 28:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Pa nyama iliyonse yoperekedwa nsembe, muziperekanso nsembe yachakumwa. Ngʼombe yamphongo muziipereka limodzi ndi vinyo+ wokwana hafu ya muyezo wa hini. Nkhosa yamphongo+ muziipereka limodzi ndi vinyo wokwana gawo limodzi mwa magawo atatu a muyezo wa hini. Ndipo mwana wa nkhosa wamphongo muzimupereka limodzi ndi vinyo wokwana gawo limodzi mwa magawo 4 a muyezo wa hini.+ Zinthu zimenezi muzizipereka monga nsembe yopsereza ya mwezi ndi mwezi ndipo muzizipereka mwezi uliwonse pa chaka.
-