Deuteronomo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Taonani, ndikukupatsani dzikolo. Mukalowe mʼdzikolo nʼkulitenga kuti likhale lanu, dziko limene Yehova analumbira kwa makolo anu, Abulahamu, Isaki+ ndi Yakobo,+ kuti adzalipereka kwa iwo ndi kwa mbadwa* zawo.’+
8 Taonani, ndikukupatsani dzikolo. Mukalowe mʼdzikolo nʼkulitenga kuti likhale lanu, dziko limene Yehova analumbira kwa makolo anu, Abulahamu, Isaki+ ndi Yakobo,+ kuti adzalipereka kwa iwo ndi kwa mbadwa* zawo.’+