Deuteronomo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Taonani, ndikukupatsani dzikolo. Mukalowe m’dzikolo ndi kulitenga kuti likhale lanu, dziko limene Yehova analumbirira makolo anu, Abulahamu, Isaki+ ndi Yakobo,+ kuti adzalipereka kwa iwo ndi kwa mbewu yawo.’+
8 Taonani, ndikukupatsani dzikolo. Mukalowe m’dzikolo ndi kulitenga kuti likhale lanu, dziko limene Yehova analumbirira makolo anu, Abulahamu, Isaki+ ndi Yakobo,+ kuti adzalipereka kwa iwo ndi kwa mbewu yawo.’+