Deuteronomo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma inu mudzawachitire zotsatirazi: Mudzagwetse maguwa awo ansembe komanso kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzadule mizati yawo yopatulika+ ndi kuwotcha zifaniziro zawo zogoba.+
5 Koma inu mudzawachitire zotsatirazi: Mudzagwetse maguwa awo ansembe komanso kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzadule mizati yawo yopatulika+ ndi kuwotcha zifaniziro zawo zogoba.+