Deuteronomo 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova dalitsani mphamvu zake,Ndipo mukondwere ndi ntchito ya manja ake. Muphwanye miyendo ya* amene akumuukira,Kuti amene amadana naye asathenso kuimirira.”
11 Inu Yehova dalitsani mphamvu zake,Ndipo mukondwere ndi ntchito ya manja ake. Muphwanye miyendo ya* amene akumuukira,Kuti amene amadana naye asathenso kuimirira.”