Deuteronomo 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova dalitsani mphamvu zake,+Ndipo mukondwere ndi ntchito ya manja ake.+Muvulaze koopsa ziuno za amene akumuukira,+Ndi amene amadana naye kwambiri, kuti asamuukire.”+
11 Inu Yehova dalitsani mphamvu zake,+Ndipo mukondwere ndi ntchito ya manja ake.+Muvulaze koopsa ziuno za amene akumuukira,+Ndi amene amadana naye kwambiri, kuti asamuukire.”+