-
1 Samueli 16:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Iye anayankha kuti: “Inde, nʼkwabwino. Ndabwera kudzapereka nsembe kwa Yehova. Dziyeretseni, ndipo tipite limodzi kopereka nsembe.” Kenako iye anayeretsa Jese ndi ana ake ndipo anawaitanira kopereka nsembe.
-