1 Samueli 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anayankha kuti: “Inde, n’kwabwino. Ndabwera kudzapereka nsembe kwa Yehova. Dziyeretseni,+ ndipo mupite nane kopereka nsembe.” Chotero iye anayeretsa Jese ndi ana ake, kenako anawaitanira kopereka nsembe.
5 Iye anayankha kuti: “Inde, n’kwabwino. Ndabwera kudzapereka nsembe kwa Yehova. Dziyeretseni,+ ndipo mupite nane kopereka nsembe.” Chotero iye anayeretsa Jese ndi ana ake, kenako anawaitanira kopereka nsembe.