-
2 Samueli 24:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma Arauna anauza Davide kuti: “Mbuyanga mfumu, tengani malowo ndipo mupereke chilichonse chimene mukuona kuti nʼchabwino. Ngʼombe iyi ikhale nsembe yopsereza ndipo chopunthira ndi zipangizo zinazi zikhale nkhuni.
-