2 Samueli 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Arauna anauza Davide kuti: “Mbuyanga mfumu, tengani+ malowo ndipo mupereke chilichonse chimene mukuona kuti n’chabwino. Onani, ng’ombe iyi ikhale nsembe yopsereza ndipo chopunthira ndi zipangizo za ng’ombe zikhale nkhuni.+
22 Koma Arauna anauza Davide kuti: “Mbuyanga mfumu, tengani+ malowo ndipo mupereke chilichonse chimene mukuona kuti n’chabwino. Onani, ng’ombe iyi ikhale nsembe yopsereza ndipo chopunthira ndi zipangizo za ng’ombe zikhale nkhuni.+