1 Mafumu 4:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ankafotokoza za mitengo, kuyambira mkungudza wa ku Lebanoni mpaka kamtengo ka hisope+ kamene kamamera pakhoma. Ankafotokozanso za zinyama,+ mbalame,+ nyama zokwawa*+ ndiponso nsomba.
33 Ankafotokoza za mitengo, kuyambira mkungudza wa ku Lebanoni mpaka kamtengo ka hisope+ kamene kamamera pakhoma. Ankafotokozanso za zinyama,+ mbalame,+ nyama zokwawa*+ ndiponso nsomba.