1 Mafumu 4:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ankafotokoza za mitengo, kuyambira mkungudza wa ku Lebanoni+ mpaka kamtengo ka hisope+ kamene kamamera pakhoma.* Ankafotokozanso za zinyama,+ zolengedwa zouluka,+ nsomba,+ ndiponso za zokwawa.+
33 Ankafotokoza za mitengo, kuyambira mkungudza wa ku Lebanoni+ mpaka kamtengo ka hisope+ kamene kamamera pakhoma.* Ankafotokozanso za zinyama,+ zolengedwa zouluka,+ nsomba,+ ndiponso za zokwawa.+