1 Mafumu 22:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova ndipo anayenda mʼnjira ya bambo ake+ ndi mayi ake+ ndiponso mʼnjira ya Yerobowamu mwana wa Nebati, amene anachititsa kuti Aisiraeli achimwe.+
52 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova ndipo anayenda mʼnjira ya bambo ake+ ndi mayi ake+ ndiponso mʼnjira ya Yerobowamu mwana wa Nebati, amene anachititsa kuti Aisiraeli achimwe.+