1 Mafumu 22:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Iye anapitiriza kuchita zoipa+ pamaso pa Yehova. Anayenda m’njira ya bambo ake,+ m’njira ya mayi ake,+ ndiponso m’njira ya Yerobowamu+ mwana wa Nebati, amene anachimwitsa Isiraeli.+
52 Iye anapitiriza kuchita zoipa+ pamaso pa Yehova. Anayenda m’njira ya bambo ake,+ m’njira ya mayi ake,+ ndiponso m’njira ya Yerobowamu+ mwana wa Nebati, amene anachimwitsa Isiraeli.+