-
2 Mafumu 9:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Munthu wokwera pahatchiyo anapitadi kukakumana ndi Yehu, nʼkunena kuti, “Mfumu yanena kuti, ‘Kodi mukubwerera zamtendere?’” Koma Yehu anati: “Ukudziwa chiyani zokhudza ‘mtendereʼ iweyo? Tiye zinditsatira!”
Ndiyeno mlonda wa pansanja uja anati: “Munthu tinamutuma uja wakumana nawo koma sakubwerera.”
-