-
2 Mafumu 9:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Chotero munthu wokwera pahatchiyo anapitadi kukakumana ndi Yehu, n’kunena kuti, “Mfumu yanena kuti, ‘Kodi mukubwerera zamtendere?’”+ Koma Yehu anati: “Ukudziwa chiyani zokhudza ‘mtendere’ iweyo? Tiye zinditsatira!”
Ndiyeno mlonda+ wa pansanja uja anati: “Munthu wauthenga tinam’tuma uja wakumana nawo koma sakubwerera.”
-