1 Mbiri 6:76 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 76 Kuchokera ku fuko la Nafitali anawapatsa mzinda wa Kedesi+ ku Galileya+ ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Hamoni ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso mzinda wa Kiriyataimu ndi malo ake odyetserako ziweto.
76 Kuchokera ku fuko la Nafitali anawapatsa mzinda wa Kedesi+ ku Galileya+ ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Hamoni ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso mzinda wa Kiriyataimu ndi malo ake odyetserako ziweto.