-
2 Mbiri 19:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndakupatsani wansembe wamkulu Amariya kuti azisamalira nkhani iliyonse yokhudza Yehova.+ Zebadiya mwana wa Isimaeli, mtsogoleri wa nyumba ya Yuda, aziyangʼanira nkhani iliyonse yokhudza mfumu. Ndakupatsaninso Alevi kuti azikuyangʼanirani. Khalani olimba mtima ndipo gwirani ntchitoyi. Yehova akhale ndi anthu amene azichita zabwino.”+
-