-
2 Mbiri 19:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndakupatsani wansembe wamkulu Amariya kuti azisamalira nkhani iliyonse yokhudza Yehova.+ Zebadiya mwana wa Isimaeli mtsogoleri wa nyumba ya Yuda aziyang’anira nkhani iliyonse yokhudza mfumu. Ndakupatsaninso Alevi kuti akhale oyang’anira anu. Khalani olimba mtima+ ndipo gwirani ntchitoyi. Yehova+ adalitse zabwino zimene muzichita.”+
-