-
2 Mbiri 24:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Atangomaliza ntchitoyo anabweretsa ndalama zimene zinatsala kwa mfumu ndi Yehoyada. Ndalamazo anazigwiritsa ntchito popanga ziwiya zamʼnyumba ya Yehova, ziwiya zogwiritsa ntchito pa utumiki ndi popereka zopereka komanso popanga makapu ndi ziwiya zagolide ndi zasiliva.+ Ndipo ankapereka nsembe zopsereza+ nthawi zonse panyumba ya Yehova masiku onse a Yehoyada.
-