-
2 Mbiri 24:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Atangomaliza ntchitoyo anabweretsa ndalama zotsalazo kwa mfumu ndi Yehoyada. Ndi ndalamazo, iwo anapanga ziwiya za nyumba ya Yehova ndiponso ziwiya zogwiritsira ntchito pa utumiki+ ndi popereka zopereka. Anapanganso makapu+ ndi ziwiya zagolide+ ndi siliva, ndipo nsembe zopsereza+ zinayamba kuperekedwa nthawi zonse m’nyumba ya Yehova masiku onse a Yehoyada.
-