2 Mbiri 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ahazi+ anakhala mfumu ali ndi zaka 20 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira Davide kholo lake.+
28 Ahazi+ anakhala mfumu ali ndi zaka 20 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira Davide kholo lake.+