2 Mbiri 34:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Komanso mfumuyo inachititsa kuti anthu onse amene anali ku Yerusalemu ndi ku Benjamini avomereze panganolo. Ndipo anthu okhala ku Yerusalemuwo anachita mogwirizana ndi pangano la Mulungu, Mulungu wa makolo awo.+
32 Komanso mfumuyo inachititsa kuti anthu onse amene anali ku Yerusalemu ndi ku Benjamini avomereze panganolo. Ndipo anthu okhala ku Yerusalemuwo anachita mogwirizana ndi pangano la Mulungu, Mulungu wa makolo awo.+