2 Mbiri 34:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kuwonjezera apo, mfumuyo inachititsa onse amene anali ku Yerusalemu ndi ku Benjamini kuti avomereze panganolo. Anthu okhala ku Yerusalemuwo anachita mogwirizana ndi pangano la Mulungu, Mulungu wa makolo awo.+
32 Kuwonjezera apo, mfumuyo inachititsa onse amene anali ku Yerusalemu ndi ku Benjamini kuti avomereze panganolo. Anthu okhala ku Yerusalemuwo anachita mogwirizana ndi pangano la Mulungu, Mulungu wa makolo awo.+