Salimo 104:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munaliphimba ndi madzi ozama ngati kuti mwaliphimba ndi nsalu.+ Madziwo anakwera kupitirira mapiri. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 104:6 Mawu a Mulungu, tsa. 100
6 Munaliphimba ndi madzi ozama ngati kuti mwaliphimba ndi nsalu.+ Madziwo anakwera kupitirira mapiri.