-
Salimo 107:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Anthu ayamike Yehova chifukwa cha chikondi chake chokhulupirika,
Ndiponso chifukwa cha ntchito zake zodabwitsa zimene wachitira ana a anthu.
-