-
Nyimbo ya Solomo 4:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mano ako ali ngati gulu la nkhosa zomwe angozimeta kumene,
Zimene zikuchokera kosambitsidwa,
Zonse zabereka mapasa,
Ndipo palibe imene ana ake afa.
-