Nyimbo ya Solomo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mano ako ali ngati gulu la nkhosa zazikazi zomwe angozimeta kumene,+ zimene zikuchokera kozisambitsa, zonse zitabereka mapasa, popanda imene ana ake afa.
2 Mano ako ali ngati gulu la nkhosa zazikazi zomwe angozimeta kumene,+ zimene zikuchokera kozisambitsa, zonse zitabereka mapasa, popanda imene ana ake afa.