Nyimbo ya Solomo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Milomo yako ili ngati chingwe chofiira kwambiri,Ndipo ukamalankhula umasangalatsa. Masaya ako munsalu yako yophimba kumutuyoAli ngati khangaza* logamphula pakati.
3 Milomo yako ili ngati chingwe chofiira kwambiri,Ndipo ukamalankhula umasangalatsa. Masaya ako munsalu yako yophimba kumutuyoAli ngati khangaza* logamphula pakati.