Nyimbo ya Solomo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Milomo yako ili ngati chingwe chofiira kwambiri, ndipo kulankhula kwako n’kosangalatsa.+ M’mbali mwa mutu wako muli ngati khangaza* logamphula pakati, munsalu yako yophimba kumutuyo.+
3 Milomo yako ili ngati chingwe chofiira kwambiri, ndipo kulankhula kwako n’kosangalatsa.+ M’mbali mwa mutu wako muli ngati khangaza* logamphula pakati, munsalu yako yophimba kumutuyo.+