Yesaya 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzakupatsani chilango,Ndidzakuyengani nʼkuchotseratu zonyansa zanu zonse,Ndidzachotsa zinthu zonse zimene zikuchititsa kuti musakhale oyera.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:25 Yesaya 1, tsa. 32-33
25 Ndidzakupatsani chilango,Ndidzakuyengani nʼkuchotseratu zonyansa zanu zonse,Ndidzachotsa zinthu zonse zimene zikuchititsa kuti musakhale oyera.+