Yesaya 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi mudzatani pa tsiku lachiweruzo,*+Anthu okuwonongani akadzabwera kuchokera kutali?+ Kodi mudzathawira kwa ndani kuti akuthandizeni+Nanga chuma* chanu mudzachisiya kuti? Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:3 Yesaya 1, ptsa. 142-143
3 Kodi mudzatani pa tsiku lachiweruzo,*+Anthu okuwonongani akadzabwera kuchokera kutali?+ Kodi mudzathawira kwa ndani kuti akuthandizeni+Nanga chuma* chanu mudzachisiya kuti?