Yesaya 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi anthu inu mudzatani pa tsiku limene adzatembenukire kwa inu+ ndi kukubweretserani chiwonongeko chochokera kutali?+ Mudzathawira kwa ndani kuti akuthandizeni+ ndipo ulemerero wanu mudzausiya kuti?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:3 Yesaya 1, ptsa. 142-143
3 Kodi anthu inu mudzatani pa tsiku limene adzatembenukire kwa inu+ ndi kukubweretserani chiwonongeko chochokera kutali?+ Mudzathawira kwa ndani kuti akuthandizeni+ ndipo ulemerero wanu mudzausiya kuti?+