Ezekieli 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ngakhale kuti anakuuzani masomphenya abodza komanso analosera zabodza zokhudza inu, anthu anu adzaunjikidwa pamodzi ndi anthu amene adzaphedwe,* omwe ndi anthu oipa amene tsiku lawo loti alandire chilango chomaliza lafika. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:29 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 20
29 Ngakhale kuti anakuuzani masomphenya abodza komanso analosera zabodza zokhudza inu, anthu anu adzaunjikidwa pamodzi ndi anthu amene adzaphedwe,* omwe ndi anthu oipa amene tsiku lawo loti alandire chilango chomaliza lafika.