Ezekieli 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 chifukwa chakuti olosera anu anakuuzani masomphenya abodza,+ chifukwa chakuti anakulosererani zabodza, kuti mukhale pagulu la anthu ophedwa, anthu oipa amene tsiku lawo loti alangidwe lafika. Mapeto a zolakwa zawo zonse afika.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:29 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 20
29 chifukwa chakuti olosera anu anakuuzani masomphenya abodza,+ chifukwa chakuti anakulosererani zabodza, kuti mukhale pagulu la anthu ophedwa, anthu oipa amene tsiku lawo loti alangidwe lafika. Mapeto a zolakwa zawo zonse afika.+