Ezekieli 47:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno anandiuza kuti: “Madzi awa akupita kuchigawo cha kumʼmawa ndipo adutsa ku Araba*+ nʼkukafika kunyanja. Madziwa akakafika kunyanjako,+ akachititsa kuti madzi amʼnyanjamo akhale abwino. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 47:8 Nsanja ya Olonda,11/1/1989, tsa. 179/15/1988, tsa. 27
8 Ndiyeno anandiuza kuti: “Madzi awa akupita kuchigawo cha kumʼmawa ndipo adutsa ku Araba*+ nʼkukafika kunyanja. Madziwa akakafika kunyanjako,+ akachititsa kuti madzi amʼnyanjamo akhale abwino.